-
Levitiko 8:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Atatero anaika zonsezi mʼmanja mwa Aroni ndi mʼmanja mwa ana ake nʼkuyamba kuziyendetsa uku ndi uku monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku yoperekedwa kwa Yehova.
-