Levitiko 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anauza Aroni kuti: “Tenga ngʼombe yaingʼono kuti ikhale nsembe yamachimo+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza. Nyama zonsezi zikhale zopanda chilema ndipo uzipereke kwa Yehova.
2 Iye anauza Aroni kuti: “Tenga ngʼombe yaingʼono kuti ikhale nsembe yamachimo+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza. Nyama zonsezi zikhale zopanda chilema ndipo uzipereke kwa Yehova.