Levitiko 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno ana ake anamubweretsera magazi+ a ngʼombeyo ndipo iye anaviika chala chake mʼmagaziwo nʼkuwapaka panyanga za guwa lansembe. Magazi otsala anawathira pansi pa guwa lansembelo.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:9 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 22
9 Ndiyeno ana ake anamubweretsera magazi+ a ngʼombeyo ndipo iye anaviika chala chake mʼmagaziwo nʼkuwapaka panyanga za guwa lansembe. Magazi otsala anawathira pansi pa guwa lansembelo.+