Levitiko 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo mafuta, impso ndi mafuta apachiwindi zimene anazitenga panyama ya nsembe yamachimo anaziwotcha paguwa lansembe, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.+
10 Ndipo mafuta, impso ndi mafuta apachiwindi zimene anazitenga panyama ya nsembe yamachimo anaziwotcha paguwa lansembe, mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.+