Levitiko 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anapereka nsembe yambewu.+ Anatapako nsembeyo kudzaza dzanja lake nʼkuiwotcha paguwa lansembe, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya mʼmawa.+
17 Kenako anapereka nsembe yambewu.+ Anatapako nsembeyo kudzaza dzanja lake nʼkuiwotcha paguwa lansembe, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya mʼmawa.+