Levitiko 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Aroni anakweza manja ake nʼkuloza anthuwo ndipo anawadalitsa.+ Atatero anatsika kuguwa lansembe atamaliza kupereka nsembe yamachimo, nsembe yopsereza ndi nsembe zamgwirizano.
22 Kenako Aroni anakweza manja ake nʼkuloza anthuwo ndipo anawadalitsa.+ Atatero anatsika kuguwa lansembe atamaliza kupereka nsembe yamachimo, nsembe yopsereza ndi nsembe zamgwirizano.