Levitiko 9:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamapeto pake Mose ndi Aroni analowa mʼchihema chokumanako, kenako anatulukamo nʼkudalitsa anthuwo.+ Atatero ulemerero wa Yehova unaonekera kwa anthu onse,+
23 Pamapeto pake Mose ndi Aroni analowa mʼchihema chokumanako, kenako anatulukamo nʼkudalitsa anthuwo.+ Atatero ulemerero wa Yehova unaonekera kwa anthu onse,+