Levitiko 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndipo moto unatsika kuchokera kwa Yehova+ nʼkunyeketsa nsembe yopsereza ndiponso mafuta, zimene zinali paguwa lansembe. Anthu onse ataona zimenezi anayamba kufuula mokondwera ndipo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+
24 ndipo moto unatsika kuchokera kwa Yehova+ nʼkunyeketsa nsembe yopsereza ndiponso mafuta, zimene zinali paguwa lansembe. Anthu onse ataona zimenezi anayamba kufuula mokondwera ndipo anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+