Levitiko 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ azikumbukira kuti ndine woyera, ndipo anthu onse adzandipatsa ulemerero.’” Koma Aroni anangokhala chete.
3 Kenako Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ azikumbukira kuti ndine woyera, ndipo anthu onse adzandipatsa ulemerero.’” Koma Aroni anangokhala chete.