Levitiko 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Mose anaitana Misayeli ndi Elizafana, ana a Uziyeli,+ bambo aangʼono a Aroni, nʼkuwauza kuti: “Bwerani muchotse abale anu patsogolo pa malo oyera, mupite nawo kunja kwa msasa.”
4 Zitatero, Mose anaitana Misayeli ndi Elizafana, ana a Uziyeli,+ bambo aangʼono a Aroni, nʼkuwauza kuti: “Bwerani muchotse abale anu patsogolo pa malo oyera, mupite nawo kunja kwa msasa.”