Levitiko 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kuopera kuti mungafe, chifukwa mwadzozedwa ndi mafuta odzozera a Yehova.”+ Choncho iwo anachita mogwirizana ndi zimene Mose ananena.
7 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kuopera kuti mungafe, chifukwa mwadzozedwa ndi mafuta odzozera a Yehova.”+ Choncho iwo anachita mogwirizana ndi zimene Mose ananena.