Levitiko 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Mukamabwera kuchihema chokumanako, iwe ndi ana ako musamamwe vinyo kapena zakumwa zina zoledzeretsa,+ kuti mungafe. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Nsanja ya Olonda,11/15/2014, tsa. 1712/1/2004, ptsa. 21-225/15/2004, tsa. 22
9 “Mukamabwera kuchihema chokumanako, iwe ndi ana ako musamamwe vinyo kapena zakumwa zina zoledzeretsa,+ kuti mungafe. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale.