-
Levitiko 10:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Iwo azibweretsa mwendo wa gawo lopatulika ndi chidale cha nsembe yoyendetsa uku ndi uku, pamodzi ndi mafuta a nsembe zowotcha pamoto, kuti woperekayo aziyendetse uku ndi uku pamaso pa Yehova. Zimenezi zizikhala gawo lanu ndi gawo la ana anu mpaka kalekale,+ mogwirizana ndi zimene Yehova walamula.”
-