Levitiko 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yamachimo,+ koma anaona kuti yonse inali itawotchedwa pamoto. Choncho iye anakwiyira Eleazara ndi Itamara, ana a Aroni amene anatsala, ndipo anati: Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda,2/15/2011, tsa. 12
16 Ndiyeno Mose anafunafuna mbuzi ya nsembe yamachimo,+ koma anaona kuti yonse inali itawotchedwa pamoto. Choncho iye anakwiyira Eleazara ndi Itamara, ana a Aroni amene anatsala, ndipo anati: