Levitiko 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Nʼchifukwa chiyani simunadye nsembe yamachimo mʼmalo oyera?+ Nsembe imeneyi ndi yopatulika koposa, ndipo Mulungu wakupatsani kuti munyamule zolakwa za gulu lonse, ndi kuphimba machimo a gulu lonseli pamaso pa Yehova. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Nsanja ya Olonda,2/15/2011, tsa. 12
17 “Nʼchifukwa chiyani simunadye nsembe yamachimo mʼmalo oyera?+ Nsembe imeneyi ndi yopatulika koposa, ndipo Mulungu wakupatsani kuti munyamule zolakwa za gulu lonse, ndi kuphimba machimo a gulu lonseli pamaso pa Yehova.