Levitiko 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani, simunabweretse magazi ake mkati, mʼmalo oyera.+ Munafunika kudya nsembeyo mʼmalo oyera, mogwirizana ndi zimene Mulungu anandilamula.” Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:18 Nsanja ya Olonda,2/15/2011, tsa. 12
18 Taonani, simunabweretse magazi ake mkati, mʼmalo oyera.+ Munafunika kudya nsembeyo mʼmalo oyera, mogwirizana ndi zimene Mulungu anandilamula.”