Levitiko 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake nʼzogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ndi yodetsedwa kwa inu.
7 Komanso nkhumba,+ chifukwa ziboda zake nʼzogawanika ndipo zili ndi mpata pakati, koma siibzikula. Ndi yodetsedwa kwa inu.