-
Levitiko 11:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Koma chilichonse chopezeka mʼnyanja ndi mʼmitsinje chimene chilibe zipsepse ndi mamba, pa zamoyo zopezeka zambiri ndi pa zamoyo zina zonse zamʼmadzi, ndi zonyansa kwa inu.
-