-
Levitiko 11:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Chamoyo chilichonse chokhala ndi mapazi a zikhadabo pa zamoyo zonse zimene zimayenda ndi miyendo yonse 4, nʼchodetsedwa kwa inu. Aliyense wokhudza chamoyo chimenechi chitafa adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.
-