-
Levitiko 11:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ndiye chilichonse cha zamoyo zimenezi chikafa nʼkugwera pa chinthu china chilichonse, chinthucho chidzakhala chodetsedwa, kaya ndi chiwiya chamtengo, chovala, chikopa kapena chiguduli. Chiwiya chilichonse chimene chimagwiritsidwa ntchito chiziviikidwa mʼmadzi, ndipo chizikhala chodetsedwa mpaka madzulo, kenako chidzakhala choyera.
-