-
Levitiko 11:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Madzi a mʼchiwiya chimenecho akagwera pachakudya chilichonse, chakudyacho chizikhala chodetsedwa. Ndipo chakumwa chilichonse chimene chili mʼchiwiya chimenecho, chidzakhala chodetsedwa.
-