Levitiko 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Aliyense amene angadye nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Aliyense amene anganyamule nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:40 Nsanja ya Olonda,7/1/2005, tsa. 27
40 Aliyense amene angadye nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.+ Aliyense amene anganyamule nyama yakufayo azichapa zovala zake, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.