Levitiko 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mkazi akakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:2 Nsanja ya Olonda,1/15/2012, tsa. 175/15/2004, tsa. 23
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Mkazi akakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, azikhala wodetsedwa kwa masiku 7. Azikhala wodetsedwa ngati mmene amakhalira pa nthawi imene akusamba.+