Levitiko 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ngati chikangacho chikuoneka choyera ndipo sichinalowe mkati mwa khungu, komanso cheya sichinasanduke choyera, wansembe azimuika munthuyo kwayekha kwa masiku 7.+
4 Koma ngati chikangacho chikuoneka choyera ndipo sichinalowe mkati mwa khungu, komanso cheya sichinasanduke choyera, wansembe azimuika munthuyo kwayekha kwa masiku 7.+