Levitiko 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ngati chikangacho chili pamalo amodzi ndipo sichinafalikire, kumeneko ndi kutukusira kwa chithupsa. Wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+
23 Koma ngati chikangacho chili pamalo amodzi ndipo sichinafalikire, kumeneko ndi kutukusira kwa chithupsa. Wansembe azigamula kuti munthuyo ndi woyera.+