-
Levitiko 13:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Munthu amene ali ndi khateyo, zovala zake zizingʼambidwa ndipo asamakonze tsitsi lake. Koma aziphimba ndevu zake zapamlomo nʼkumafuula kuti, ‘Wodetsedwa, wodetsedwa!’
-