-
Levitiko 13:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 ndipo nthendayo ikuoneka yobiriwira mopitira ku chikasu kapena yofiirira pachovala kapena pachikopa, mulitali kapena mulifupi mwa nsalu, kapena pachinthu chilichonse chopangidwa ndi chikopa, imeneyo ndi nthenda ya khate ndipo chinthucho muyenera kukachionetsa kwa wansembe.
-