Levitiko 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 wansembe azimulamula kuti abweretse mbalame zamoyo ziwiri zosadetsedwa, nthambi ya mtengo wa mkungudza, ulusi wofiira kwambiri ndi kamtengo ka hisope* kuti adzazigwiritse ntchito pomuyeretsa.+
4 wansembe azimulamula kuti abweretse mbalame zamoyo ziwiri zosadetsedwa, nthambi ya mtengo wa mkungudza, ulusi wofiira kwambiri ndi kamtengo ka hisope* kuti adzazigwiritse ntchito pomuyeretsa.+