Levitiko 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako wansembe azidontheza magaziwo maulendo 7 pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera. Akatero aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+
7 Kenako wansembe azidontheza magaziwo maulendo 7 pamunthu amene akudziyeretsa ku khateyo, ndipo azigamula kuti munthuyo ndi woyera. Akatero aziulutsa mbalame yamoyo ija pabwalo.+