-
Levitiko 14:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Ndipo wansembe amene wagamula kuti munthuyo ndi woyera, azionetsa amene akudziyeretsayo, limodzi ndi zinthu zakezo kwa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako.
-