Levitiko 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wansembeyo azidzatenga nkhosa yaingʼono yamphongo imodzi nʼkuipereka monga nsembe yakupalamula+ pamodzi ndi muyezo umodzi wa mafuta uja. Zimenezi aziziyendetsa uku ndi uku monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova.+
12 Wansembeyo azidzatenga nkhosa yaingʼono yamphongo imodzi nʼkuipereka monga nsembe yakupalamula+ pamodzi ndi muyezo umodzi wa mafuta uja. Zimenezi aziziyendetsa uku ndi uku monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova.+