Levitiko 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku la 8+ azibweretsa zinthuzi kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako pamaso pa Yehova,+ kuti wansembeyo agamule kuti munthuyo ndi woyera.
23 Pa tsiku la 8+ azibweretsa zinthuzi kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako pamaso pa Yehova,+ kuti wansembeyo agamule kuti munthuyo ndi woyera.