Levitiko 14:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako wansembe azitenga nkhosa yaingʼono yamphongo ya nsembe yakupalamula+ ndi muyezo umodzi wa mafuta uja, ndipo wansembeyo aziyendetsa zinthu zimenezi uku ndi uku, monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova.+
24 Kenako wansembe azitenga nkhosa yaingʼono yamphongo ya nsembe yakupalamula+ ndi muyezo umodzi wa mafuta uja, ndipo wansembeyo aziyendetsa zinthu zimenezi uku ndi uku, monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova.+