Levitiko 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza,+ azipereka imene angakwanitse pamodzi ndi nsembe yambewu. Ndipo wansembe aziphimba machimo a munthu amene akudziyeretsayo pamaso pa Yehova.+
31 Mbalame imodzi ikhale nsembe yamachimo ndipo inayo ikhale nsembe yopsereza,+ azipereka imene angakwanitse pamodzi ndi nsembe yambewu. Ndipo wansembe aziphimba machimo a munthu amene akudziyeretsayo pamaso pa Yehova.+