-
Levitiko 14:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Limeneli ndi lamulo lokhudza munthu amene ali ndi nthenda ya khate, amene sangakwanitse kupeza zinthu zimene zimafunika pa tsiku la kuyeretsedwa kwake.”
-