Levitiko 14:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndiyeno kuti ayeretse nyumbayo, azitenga mbalame ziwiri, nthambi ya mtengo wa mkungudza, ulusi wofiira kwambiri ndi kamtengo ka hisope.+
49 Ndiyeno kuti ayeretse nyumbayo, azitenga mbalame ziwiri, nthambi ya mtengo wa mkungudza, ulusi wofiira kwambiri ndi kamtengo ka hisope.+