-
Levitiko 15:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Aliyense wokhala pachinthu chimene munthu amene akukhayo anakhalapo, azichapa zovala zake ndi kusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.
-