Levitiko 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngati munthu amene akukhayo+ wagwira munthu wina asanasambe mʼmanja, munthuyo azichapa zovala zake nʼkusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.
11 Ngati munthu amene akukhayo+ wagwira munthu wina asanasambe mʼmanja, munthuyo azichapa zovala zake nʼkusamba thupi lonse, ndipo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.