Levitiko 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda+ ndipo azibwera nazo pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako, nʼkuzipereka kwa wansembe.
14 Pa tsiku la 8 azitenga njiwa ziwiri kapena ana awiri a nkhunda+ ndipo azibwera nazo pamaso pa Yehova, pakhomo la chihema chokumanako, nʼkuzipereka kwa wansembe.