Levitiko 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Akasiya kukha magaziwo, pazipita masiku 7, kenako azikhala woyera.+