Levitiko 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Aroni azibweretsa ngʼombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, ndipo aziphimba machimo ake ndi a banja lake. Pambuyo pake azipha ngʼombe ya nsembe yake yamachimoyo.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:11 Nsanja ya Olonda,2/15/1998, ptsa. 12, 17
11 Aroni azibweretsa ngʼombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, ndipo aziphimba machimo ake ndi a banja lake. Pambuyo pake azipha ngʼombe ya nsembe yake yamachimoyo.+