Levitiko 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Lamulo limeneli laperekedwa kuti nsembe zimene Aisiraeli akuzipereka kunja, azibwera nazo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako kuti azipereke kwa Yehova. Zimenezi ziziperekedwa monga nsembe zamgwirizano kwa Yehova.+
5 Lamulo limeneli laperekedwa kuti nsembe zimene Aisiraeli akuzipereka kunja, azibwera nazo kwa wansembe pakhomo la chihema chokumanako kuti azipereke kwa Yehova. Zimenezi ziziperekedwa monga nsembe zamgwirizano kwa Yehova.+