Levitiko 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usagone ndi mkazi wa bambo ako,+ chifukwa kuchita zimenezo nʼkuchititsa manyazi bambo ako.*