Levitiko 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usagone ndi mkazi wa mchimwene wako,+ chifukwa kumeneko nʼkuchititsa manyazi* mchimwene wako.