Levitiko 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usagone ndi mkazi limodzi ndi mwana wake wamkazi.+ Usatenge mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wa mkazi wakoyo komanso mwana wamkazi wa mwana wake wamkazi kuti ugone naye. Limeneli ndi khalidwe lonyansa* chifukwa amenewa ndi achibale a mkazi wako.
17 Usagone ndi mkazi limodzi ndi mwana wake wamkazi.+ Usatenge mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wa mkazi wakoyo komanso mwana wamkazi wa mwana wake wamkazi kuti ugone naye. Limeneli ndi khalidwe lonyansa* chifukwa amenewa ndi achibale a mkazi wako.