Levitiko 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe* kwa Moleki.+ Usanyoze dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi.+ Ine ndine Yehova.
21 Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe* kwa Moleki.+ Usanyoze dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi.+ Ine ndine Yehova.