Levitiko 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwamuna asamagone ndi nyama nʼkukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asamadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kuchita zimenezi nʼkosemphana ndi chibadwa. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:23 Nsanja ya Olonda,7/15/2003, tsa. 27
23 Mwamuna asamagone ndi nyama nʼkukhala wodetsedwa, ndipo mkazi asamadzipereke kwa nyama kuti agone nayo.+ Kuchita zimenezi nʼkosemphana ndi chibadwa.