Levitiko 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Musamadzidetse ndi chilichonse cha zinthu zimenezi, chifukwa mitundu imene ndikuithamangitsa pamaso panu yadzidetsa ndi makhalidwe onyansawa.+
24 Musamadzidetse ndi chilichonse cha zinthu zimenezi, chifukwa mitundu imene ndikuithamangitsa pamaso panu yadzidetsa ndi makhalidwe onyansawa.+