Levitiko 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa anthu amene ankakhala mʼdzikolo inu musanafike ankachita zinthu zonyansa zimenezi,+ ndipo panopa dzikolo ndi lodetsedwa.
27 Chifukwa anthu amene ankakhala mʼdzikolo inu musanafike ankachita zinthu zonyansa zimenezi,+ ndipo panopa dzikolo ndi lodetsedwa.