Levitiko 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka kapena munthu wolemera.+ Ndipo muziweruza mwachilungamo.
15 Musamaweruze mopanda chilungamo. Musamakondere munthu wosauka kapena munthu wolemera.+ Ndipo muziweruza mwachilungamo.